Prières en chewa | Dominik M. Ramík Dominik M. Ramík
Česky
In English


Prières en chewa (chicheŵa)

list Afficher la liste des prières en toutes les langues





autorenewChargement de la carte
 Langue vivante (126)   Langue en danger (12)   Langue moribonde / morte (4)
 Locuteur en dehors de la zone habituelle de la langue


Vous aimez ce projet? Soutenez le par une donation via PayPal.

Chewa, nyanja (chicheŵa)

face Locuteur: Dominic (Malawi, Lilongwe)
add_circle_outline Église: Église catholique (romaine)
translate Plus d'information sur la langue: text_fields Écriture: latin (info sur ScriptSource)
import_contacts Origine du texte: Le texte vient des ressources officielles de l'église.

Signe de la Croix en chewa (chicheŵa)

play_circle_filled
Mdzina la Atate, ndi la Mwana ndi la Mzimu Woyera. Amen

Notre Père en chewa (chicheŵa)

play_circle_filled
Atate athu muli m'mwamba,
dzina lanu liyeretsedwe,
ufumu wanu udze,
kufuna kwanu kuchitidwe,
monga kumwamba choncho pansi pano. 
Mutipatse ife lero chakudya chathu cha lero. 
Mutikhululukire ife zochimwa zathu,
monga ifenso tiakhululukira adani athu,
musatisiye ife m'chinyengo,
koma mutipulumutse ife kwa zoyipa.
Amen

Je vous salue Marie en chewa (chicheŵa)

play_circle_filled
Tikuoneni Maria wa chaulele chodzadza,
Ambuye ali nanu.
Ndinu odala kopambana akazi onse,
Ndipo mngodalanso mwana wanu Yesu.
Maria oyera amayi a mulungu
mutipempherere ife ochimwa,
Tsopano ndiponso pa nthawi yakufa kwathu.
Amen

Gloire au Père en chewa (chicheŵa)

play_circle_filled
Ulemu ukhale kwa Atate, ndi kwa Mwana ndi kwa Mzimu Woyera,
monga panali poyamba ndi tsopano ndi masiku onse, ndi pa nthawi zosatha.
Amen

Symbole des Apôtres en chewa (chicheŵa)

play_circle_filled
Ine ndimvera Mulungu Atate wamphamvu zonse,
amene analenga Dziko la kumwamba ndi dziko la pansi pano.
Ndipo Yesu Khristu Mwana wake yekha, Ambuye athu,
amene anayikidwa m'mimba ndi Mzimu Woyera,
nabadwa mwa Maria Virigo,
adamsautsa kwa Ponsio Pilato.
Adampachika pamtanda, anamwalira, adamuyika m'manda,
adalowa m'limbo, ndipo mkuja wake adauka kwa akufa,
nakwera kumwamba nakhala padzanja lamanja la Mulungu Atate Amphamvu zonse.
Adzafumira komweko kudzaweruza amoyo ndi akufa.
Ndipo ndimvera Mzimu Woyera,
Eklezia Katolika Woyera,
ndimveranso kuti Oyera ayanjana,
Mulungu atikhululukira machimo,
thupi lidzauka,
ulipo moyo osatha.
Amen
list Afficher la liste des prières en toutes les langues



Vanuatu